Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 3:22 - Buku Lopatulika

22 Owerengedwa ao, powawerenga amuna onse, kuyambira mwana wa mwezi umodzi ndi mphambu, owerengedwa ao ndiwo zikwi zisanu ndi ziwiri mphambu mazana asanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Owerengedwa ao, powawerenga amuna onse, kuyambira mwana wa mwezi umodzi ndi mphambu, owerengedwa ao ndiwo zikwi zisanu ndi ziwiri mphambu mazana asanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Chiŵerengero chao potsata kuchuluka kwa amuna onse, kuyambira mwana wamwamuna wa mwezi umodzi ndi wopitirapo, chinali 7,500.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Chiwerengero cha amuna onse amene anawawerenga a mwezi umodzi kapena kupitirirapo chinali 7,500.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 3:22
3 Mawu Ofanana  

Banja la Libini, ndi mabanja a Simei, ndiwo a Geresoni; ndiwo mabanja a Geresoni.


Mabanja a Ageresoni azimanga mahema ao pambuyo pa chihema kumadzulo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa