Ndinafuulira kwa inu, Yehova; ndinati, Inu ndinu pothawirapo panga, gawo langa m'dziko la amoyo.
Masalimo 143:9 - Buku Lopatulika Mundilanditse kwa adani anga, Yehova; ndibisala mwa Inu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mundilanditse kwa adani anga, Yehova; ndibisala mwa Inu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Inu Chauta, pulumutseni kwa adani anga, chifukwa ndathaŵira kwa Inu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pulumutseni kwa adani anga, Inu Yehova, pakuti ndimabisala mwa Inu. |
Ndinafuulira kwa inu, Yehova; ndinati, Inu ndinu pothawirapo panga, gawo langa m'dziko la amoyo.
Tulutsani moyo wanga m'ndende, kuti ndiyamike dzina lanu; olungama adzandizinga; pakuti mudzandichitira zokoma.
Nyengo zanga zili m'manja mwanu, mundilanditse m'manja a adani anga, ndi kwa iwo akundilondola ine.
Pamenepo adani anga adzabwerera m'mbuyo tsiku lakuitana ine. Ichi ndidziwa, kuti Mulungu avomerezana nane.
kuti mwa zinthu ziwiri zosasinthika, m'mene Mulungu sangathe kunama, tikakhale nacho chotichenjeza cholimba, ife amene tidathawira kuchigwira chiyembekezo choikika pamaso pathu;