Masalimo 143:10 - Buku Lopatulika10 Mundiphunzitse chokonda Inu; popeza Inu ndinu Mulungu wanga; Mzimu wanu ndi wokoma; munditsogolere kuchidikha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Mundiphunzitse chokonda Inu; popeza Inu ndinu Mulungu wanga; Mzimu wanu ndi wokoma; munditsogolere kuchidikha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Phunzitseni, kuti ndizichita zofuna Inu, pakuti ndinu Mulungu wanga. Mzimu wanu wabwino unditsogolere pa njira yanu yosalala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Phunzitseni kuchita chifuniro chanu, popeza ndinu Mulungu wanga; Mzimu wanu wabwino unditsogolere pa njira yanu yosalala. Onani mutuwo |