Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 143:9 - Buku Lopatulika

9 Mundilanditse kwa adani anga, Yehova; ndibisala mwa Inu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Mundilanditse kwa adani anga, Yehova; ndibisala mwa Inu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Inu Chauta, pulumutseni kwa adani anga, chifukwa ndathaŵira kwa Inu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Pulumutseni kwa adani anga, Inu Yehova, pakuti ndimabisala mwa Inu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 143:9
10 Mawu Ofanana  

Ndinafuulira kwa inu, Yehova; ndinati, Inu ndinu pothawirapo panga, gawo langa m'dziko la amoyo.


Tulutsani moyo wanga m'ndende, kuti ndiyamike dzina lanu; olungama adzandizinga; pakuti mudzandichitira zokoma.


Nyengo zanga zili m'manja mwanu, mundilanditse m'manja a adani anga, ndi kwa iwo akundilondola ine.


Pamenepo adani anga adzabwerera m'mbuyo tsiku lakuitana ine. Ichi ndidziwa, kuti Mulungu avomerezana nane.


Ndidzafuulira kwa Mulungu Wam'mwambamwamba; ndiye Mulungu wonditsirizira zonse.


Ndilanditseni kwa adani anga, Mulungu wanga, ndiikeni pamsanje kwa iwo akundiukira.


Dzina la Yehova ndilo nsanja yolimba; wolungama athamangiramo napulumuka.


kuti mwa zinthu ziwiri zosasinthika, m'mene Mulungu sangathe kunama, tikakhale nacho chotichenjeza cholimba, ife amene tidathawira kuchigwira chiyembekezo choikika pamaso pathu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa