Masalimo 142:7 - Buku Lopatulika7 Tulutsani moyo wanga m'ndende, kuti ndiyamike dzina lanu; olungama adzandizinga; pakuti mudzandichitira zokoma. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Tulutsani moyo wanga m'ndende, kuti ndiyamike dzina lanu; olungama adzandizinga; pakuti mudzandichitira zokoma. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tulutseni m'ndende kuti ndizitamanda dzina lanu. Anthu anu adzandizungulira, chifukwa Inu mwandichitira zabwino zambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Tulutseni mʼndende yanga kuti nditamande dzina lanu. Ndipo anthu olungama adzandizungulira chifukwa cha zabwino zanu pa ine. Onani mutuwo |