Masalimo 142:6 - Buku Lopatulika6 Tamverani kufuula kwanga; popeza ndisauka kwambiri; ndilanditseni kwa iwo akundilondola; popeza andipambana. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Tamverani kufuula kwanga; popeza ndisauka kwambiri; ndilanditseni kwa iwo akundilondola; popeza andilaka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Imvani kulira kwanga, pakuti ndataya mtima. Pulumutseni kwa ondizunza, chifukwa andiposa mphamvu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Mverani kulira kwanga pakuti ndathedwa nzeru; pulumutseni kwa amene akundithamangitsa pakuti ndi amphamvu kuposa ine. Onani mutuwo |