Masalimo 57:2 - Buku Lopatulika2 Ndidzafuulira kwa Mulungu Wam'mwambamwamba; ndiye Mulungu wonditsirizira zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndidzafuulira kwa Mulungu Wam'mwambamwamba; ndiye Mulungu wonditsirizira zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ndikulirira Mulungu Wopambanazonse, Mulungu amene amandichitiradi zonse zimene walonjeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ine ndikufuwulira kwa Mulungu Wammwambamwamba, kwa Mulungu amene amakwaniritsa cholinga chake pa ine. Onani mutuwo |