Masalimo 127:4 - Buku Lopatulika Ana a ubwana wake wa munthu akunga mivi m'dzanja lake la chiphona. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ana a ubwana wake wa munthu akunga mivi m'dzanja lake la chiphona. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ana apaunyamata ali ngati mivi m'manja mwa munthu wankhondo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ana a pa unyamata ali ngati mivi mʼmanja mwa munthu wankhondo. |
Pakuti, taonani, ndidzabukitsa ndidzafikitsa kudzamenyana ndi Babiloni msonkhano wa mitundu yaikulu kuchokera kudziko la kumpoto; ndipo adzaguba pomenyana ndi iye; kumeneko Babiloni adzachotsedwa; mivi yao idzakhala ngati ya munthu wamaluli wamphamvu; yosabwera chabe.