Masalimo 127:3 - Buku Lopatulika3 Taonani, ana ndiwo cholowa cha kwa Yehova; chipatso cha m'mimba ndicho mphotho yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Taonani, ana ndiwo cholandira cha kwa Yehova; chipatso cha m'mimba ndicho mphotho yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Zoonadi, ana ndi mphatso yochokera kwa Chauta, zidzukulu ndi mphotho yake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ana ndiye cholowa chochokera kwa Yehova, ana ndi mphotho yochokera kwa Iye. Onani mutuwo |