Masalimo 127:5 - Buku Lopatulika5 Wodala munthu amene anadzaza nayo phodo lake: sadzachita manyazi iwo, pakulankhula nao adani kuchipata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Wodala munthu amene anadzaza nayo phodo lake: sadzachita manyazi iwo, pakulankhula nao adani kuchipata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ngwodala amene phodo lake nlodzaza ndi mivi yotere. Sadzamchititsa manyazi akamalankhula ndi adani ake pa bwalo lamilandu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Wodala munthu amene motengera mivi mwake mwadzaza. Iwo sadzachititsidwa manyazi pamene alimbana ndi adani awo pa zipata. Onani mutuwo |