Masalimo 127:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Wodala munthu amene motengera mivi mwake mwadzaza. Iwo sadzachititsidwa manyazi pamene alimbana ndi adani awo pa zipata. Onani mutuwoBuku Lopatulika5 Wodala munthu amene anadzaza nayo phodo lake: sadzachita manyazi iwo, pakulankhula nao adani kuchipata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Wodala munthu amene anadzaza nayo phodo lake: sadzachita manyazi iwo, pakulankhula nao adani kuchipata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ngwodala amene phodo lake nlodzaza ndi mivi yotere. Sadzamchititsa manyazi akamalankhula ndi adani ake pa bwalo lamilandu. Onani mutuwo |