Ndipo iye anati, Ndikupatsa iwe bwanji? Ndipo Yakobo anati, Usandipatse ine kanthu; ukandichitira ine chotero, ine ndidzadyetsanso ndi kusunganso ziweto zako.
Masalimo 118:8 - Buku Lopatulika Kuthawira kwa Yehova nkokoma koposa kukhulupirira munthu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Kuthawira kwa Yehova nkokoma koposa kukhulupirira munthu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Kuthaŵira kwa Chauta nkwabwino kupambana kukhulupirira munthu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Nʼkwabwino kuthawira kwa Yehova kusiyana ndi kudalira munthu. |
Ndipo iye anati, Ndikupatsa iwe bwanji? Ndipo Yakobo anati, Usandipatse ine kanthu; ukandichitira ine chotero, ine ndidzadyetsanso ndi kusunganso ziweto zako.
Wodala munthuyo wakuyesa Yehova wokhulupirika; wosasamala odzikuza, ndi opatukira kubodza.