Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 118:9 - Buku Lopatulika

9 Kuthawira kwa Yehova nkokoma koposa kukhulupirira akulu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Kuthawira kwa Yehova nkokoma koposa kukhulupirira akulu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Kuthaŵira kwa Chauta nkwabwino kupambana kukhulupirira mafumu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Nʼkwabwino kuthawira kwa Yehova kusiyana ndi kudalira mafumu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 118:9
8 Mawu Ofanana  

Tsoka kwa iwo amene atsikira kunka ku Ejipito kukathandizidwa, natama akavalo; nakhulupirira magaleta, pakuti ali ambiri, ndi okwera pa akavalo, pakuti ali a mphamvu zambiri; koma sayang'ana Woyera wa Israele, ngakhale kumfuna Yehova!


Pamenepo Asiriya adzagwa ndi lupanga losati la munthu; ndi lupanga losati la anthu lidzammaliza iye; ndipo iye adzathawa lupanga, ndi anyamata ake adzalamba.


Muja anakugwira ndi dzanja unathyoka, ndi kulasa mapewa ao onse; ndi muja anakutsamira unathyoka, ndi kuwagwedeza ziuno zao zonse.


Pakuti tsopano adzati, Tilibe mfumu, popeza sitiopa Yehova; ndi mfumu idzatichitira chiyani?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa