Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 118:10 - Buku Lopatulika

10 Amitundu onse adandizinga, zedi, m'dzina la Yehova ndidzawaduladula.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Amitundu onse adandizinga, zedi, m'dzina la Yehova ndidzawaduladula.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Adani a mitundu yonse adandizinga, koma ndidaŵaononga ndi mphamvu za dzina la Chauta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Anthu a mitundu yonse anandizinga, koma mʼdzina la Yehova ndinawawononga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 118:10
12 Mawu Ofanana  

Ndipo adani anga mwawalozetsa m'mbuyo kwa ine, kuti ndipasule ondidawo.


Anafuula, koma panalibe wopulumutsa; ngakhale kwa Yehova, koma sanawavomereze.


Zinandizungulira ngati madzi tsiku lonse; zinandizinga pamodzi.


Munandichotsera kutali wondikonda ndi bwenzi langa, odziwana nane akhala kumdima.


Ndipo kudzachitika tsiku ilo, ndidzaika Yerusalemu akhale mwala wolemetsa mitundu yonse ya anthu; onse akuusenza adzadzilasa nao; ndi amitundu onse a padziko lapansi adzasonkhana kutsutsana nao.


Ndipo mafumu awa onse anasonkhana, nadza namanga pamodzi ku madzi a Meromu, kumthira Israele nkhondo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa