Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 118:11 - Buku Lopatulika

11 Adandizinga, inde, adandizinga: Indedi, m'dzina la Yehova ndidzawaduladula.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Adandizinga, inde, adandizinga: Indedi, m'dzina la Yehova ndidzawaduladula.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Adandizinga, inde adandizinga pa mbali zonse, koma ndidaŵaononga ndi mphamvu za dzina la Chauta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Anandizinga mbali zonse, koma mʼdzina la Yehova ndinawawononga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 118:11
6 Mawu Ofanana  

Pakuona Yowabu tsono kuti nkhondo inamdzera kumaso ndi kumbuyo, anasankha amuna osankhika onse a Israele, nawanika ayambane ndi Aaramu.


Anafuula, koma panalibe wopulumutsa; ngakhale kwa Yehova, koma sanawavomereze.


Zinandizungulira ngati madzi tsiku lonse; zinandizinga pamodzi.


Munandichotsera kutali wondikonda ndi bwenzi langa, odziwana nane akhala kumdima.


Ndipo Saulo anamuka mbali ina ya phiri, Davide ndi anthu ake kuseri kwake; ndipo Davide anafulumira kuthawa, chifukwa cha kuopa Saulo; popeza Saulo ndi anthu ake anazinga Davide ndi anthu ake kwete kuti awagwire.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa