Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 118:8 - Buku Lopatulika

8 Kuthawira kwa Yehova nkokoma koposa kukhulupirira munthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Kuthawira kwa Yehova nkokoma koposa kukhulupirira munthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Kuthaŵira kwa Chauta nkwabwino kupambana kukhulupirira munthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Nʼkwabwino kuthawira kwa Yehova kusiyana ndi kudalira munthu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 118:8
6 Mawu Ofanana  

Ndipo iye anati, Ndikupatsa iwe bwanji? Ndipo Yakobo anati, Usandipatse ine kanthu; ukandichitira ine chotero, ine ndidzadyetsanso ndi kusunganso ziweto zako.


Musamakhulupirira zinduna, kapena mwana wa munthu, amene mulibe chipulumutso mwa iye.


Wodala munthuyo wakuyesa Yehova wokhulupirika; wosasamala odzikuza, ndi opatukira kubodza.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa