Masalimo 40:4 - Buku Lopatulika4 Wodala munthuyo wakuyesa Yehova wokhulupirika; wosasamala odzikuza, ndi opatukira kubodza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Wodala munthuyo wakuyesa Yehova wokhulupirika; wosasamala odzikuza, ndi opatukira kubodza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ngwodala munthu amene amadalira Chauta, munthu amene sapatukira ku mafano kapena kutsata milungu yonama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ndi wodala munthu amakhulupirira Yehova; amene sayembekezera kwa odzikuza, kapena kwa amene amatembenukira kwa milungu yabodza. Onani mutuwo |