Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 30:31 - Buku Lopatulika

31 Ndipo iye anati, Ndikupatsa iwe bwanji? Ndipo Yakobo anati, Usandipatse ine kanthu; ukandichitira ine chotero, ine ndidzadyetsanso ndi kusunganso ziweto zako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

31 Ndipo iye anati, Ndikupatsa iwe bwanji? Ndipo Yakobo anati, Usandipatse ine kanthu; ukandichitira ine chotero, ine ndidzadyetsanso ndi kusunganso ziweto zako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

31 Apo Labani adamufunsa kuti, “Kodi ndikulipire chiyani?” Yakobe adayankha kuti, “Sindifuna malipiro ena aliwonse. Komabe ndidzapitirira kukuŵeterani zoŵeta zanu, mukavomera kuchita zimene ndinene.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

31 Labani anafunsa, “Ndikupatse chiyani?” Yakobo anayankha, “Musandipatse kanthu. Koma mungondichitira izi ndipo ndidzapitiriza kusamalira nkhosa zanu ndi kuziyangʼanira:

Onani mutuwo Koperani




Genesis 30:31
5 Mawu Ofanana  

Chifukwa ndisadafike ine, iwe unali nazo zowerengeka, ndipo zachuluka zambirimbiri; Yehova wakudalitsa iwe kulikonse ndinayendako: tsopano ndidzamanga liti banja langa?


Ndidzapita ine lero pakati pa ziweto zonse kusankhasankha m'menemo zoweta zonse zamathothomathotho ndi zamawangamawanga, ndi za nkhosa zonse, ndi mbuzi zonse zamawangamawanga ndi zamathothomathotho: zotero zidzakhala malipiro anga.


Kuthawira kwa Yehova nkokoma koposa kukhulupirira munthu.


Mtima wanu ukhale wosakonda chuma; zimene muli nazo zikukwanireni; pakuti Iye anati, Sindidzakusiya konse, kungakhale kukutaya, sindidzakutaya ndithu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa