Masalimo 146:3 - Buku Lopatulika3 Musamakhulupirira zinduna, kapena mwana wa munthu, amene mulibe chipulumutso mwa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Musamakhulupirira zinduna, kapena mwana wa munthu, amene mulibe chipulumutso mwa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Musakhulupirire mafumu kapena anthu ena amene sangathe kuthandiza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Musamadalire mafumu, anthu osakhalitsa, amene sangathe kupulumutsa. Onani mutuwo |