Masalimo 146:2 - Buku Lopatulika2 Ndidzalemekeza Yehova m'moyo mwanga; ndidzaimbira zomlemekeza Mulungu wanga pokhala ndi moyo ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndidzalemekeza Yehova m'moyo mwanga; ndidzaimbira zomlemekeza Mulungu wanga pokhala ndi moyo ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ndidzatamanda Chauta pa moyo wanga wonse. Ndidzaimba nyimbo zotamanda Mulungu wanga nthaŵi zonse pamene ndili moyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndidzatamanda Yehova ndi moyo wanga wonse; ndidzayimba nyimbo zamatamando kwa Mulungu wanga nthawi yonse ya moyo wanga. Onani mutuwo |