Genesis 26:13 - Buku Lopatulika Ndipo analemera munthuyo, nalemera ndithu kufikira kuti anakhala wolemera kwambiri: Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo analemera munthuyo, nalemera ndithu kufikira kuti anakhala wolemera kwambiri: Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Chuma chake chidanka chichulukirachulukira, ndipo adasanduka munthu wolemera kwambiri. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Isake analemera. Chuma chake chinkachulukirachulukira mpaka anasanduka munthu wolemera kwambiri. |
Yehova wamdalitsa mbuyanga kwambiri; ndipo analemera kwakulukulu; ndipo anampatsa iye nkhosa ndi ng'ombe, ndi siliva ndi golide, ndi akapolo ndi adzakazi, ndi ngamira ndi abulu.
Munthuyo ndipo analemera kwambiri, nali nazo zoweta zambiri, ndi akapolo aamuna ndi aakazi, ndi ngamira, ndi abulu.
M'nyumba mwake mudzakhala akatundu ndi chuma: Ndi chilungamo chake chikhala chikhalire.