Genesis 26:14 - Buku Lopatulika14 ndipo anali ndi chuma cha nkhosa, ndi chuma cha zoweta, ndi banja lalikulu: ndipo Afilisti anamchitira iye nsanje. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 ndipo anali ndi chuma cha nkhosa, ndi chuma cha zoweta, ndi banja lalikulu: ndipo Afilisti anamchitira iye nsanje. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Afilisti adayamba kuchita naye kaduka, chifukwa choti anali ndi nkhosa ndi ng'ombe zambiri, pamodzi ndi akapolo ochuluka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Anali ndi nkhosa, ngʼombe ndi antchito ambiri mwakuti Afilisti anamuchitira nsanje. Onani mutuwo |