Genesis 26:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo zitsime zonse anakumba anyamata a atate wake, Abrahamuyo akali moyo, Afilisti anazitseka, nazikwirira ndi dothi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo zitsime zonse anakumba anyamata a atate wake, Abrahamuyo akali moyo, Afilisti anazitseka, nazikwirira ndi dothi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 (Anthuwo anali atakwirira zitsime zonse zimene antchito a bambo wake Abrahamu adaakumba, Abrahamuyo adakali ndi moyo.) Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Nthawi iyi nʼkuti Afilisti atakwirira ndi dothi zitsime zonse zimene antchito abambo ake Abrahamu anakumba mu nthawi ya abambo akewo. Onani mutuwo |