Genesis 26:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo Abimeleki anati kwa Isaki, Uchoke kwa ife chifukwa kuti iwe uli wamphamvu wopambana ife. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo Abimeleki anati kwa Isaki, Uchoke kwa ife chifukwa kuti iwe uli wamphamvu wopambana ife. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono Abimeleki adauza Isaki kuti, “Muchoke kuno. Inu ndinu amphamvu kupambana ife.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ndipo Abimeleki anati kwa Isake, “Muchoke pakati pathu chifukwa mwasanduka wamphamvu kuposa ife.” Onani mutuwo |