Genesis 26:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo Isaki anachoka kumeneko, namanga hema wake m'chigwa cha Gerari, nakhala kumeneko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo Isaki anachoka kumeneko, namanga hema wake m'chigwa cha Gerari, nakhala kumeneko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Motero Isaki adachoka nakamanga mahema m'chigwa cha Gerari nakhazikikako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Choncho Isake anachokako kumeneko nakakhala ku chigwa cha Gerari kumene anakhazikikako. Onani mutuwo |