Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 26:13 - Buku Lopatulika

13 Ndipo analemera munthuyo, nalemera ndithu kufikira kuti anakhala wolemera kwambiri:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndipo analemera munthuyo, nalemera ndithu kufikira kuti anakhala wolemera kwambiri:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Chuma chake chidanka chichulukirachulukira, ndipo adasanduka munthu wolemera kwambiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Isake analemera. Chuma chake chinkachulukirachulukira mpaka anasanduka munthu wolemera kwambiri.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 26:13
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Abramu anali wolemera ndithu ndi ng'ombe ndi siliva ndi golide.


Yehova wamdalitsa mbuyanga kwambiri; ndipo analemera kwakulukulu; ndipo anampatsa iye nkhosa ndi ng'ombe, ndi siliva ndi golide, ndi akapolo ndi adzakazi, ndi ngamira ndi abulu.


Munthuyo ndipo analemera kwambiri, nali nazo zoweta zambiri, ndi akapolo aamuna ndi aakazi, ndi ngamira, ndi abulu.


M'nyumba mwake mudzakhala akatundu ndi chuma: Ndi chilungamo chake chikhala chikhalire.


Madalitso a Yehova alemeretsa, saonjezerapo chisoni.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa