Eksodo 21:26 - Buku Lopatulika
Munthu akampanda mnyamata wake, kapena mdzakazi wake, padiso, nalithudzula, azimlola amuke waufulu chifukwa cha diso lake.
Onani mutuwo
Munthu akampanda mnyamata wake, kapena mdzakazi wake, padiso, nalithudzula, azimlola amuke waufulu chifukwa cha diso lake.
Onani mutuwo
“Munthu akamenya kapolo wamwamuna kapena wamkazi pa diso, nkulikoloola disolo, ammasule kapoloyo, kuti akhale mfulu chifukwa cha disolo.
Onani mutuwo
“Ngati munthu amenya wantchito wake wa mwamuna kapena mdzakazi wake pa diso ndi kuliwononga, wantchitoyo amasulidwe ngati malipiro a diso lake.
Onani mutuwo