Eksodo 21:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo akagulula dzino la mnyamata wake, kapena dzino la mdzakazi wake, azimlola amuke waufulu chifukwa cha dzino lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo akagulula dzino la mnyamata wake, kapena dzino la mdzakazi wake, azimlola amuke waufulu chifukwa cha dzino lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Akamchotsa dzino, ammasule kapoloyo, kuti akhale mfulu chifukwa cha dzinolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Ndipo ngati agulula dzino la wantchito wamwamuna kapena mdzakazi, wantchitoyo amasulidwe ngati malipiro a dzino lake. Onani mutuwo |