Masalimo 9:12 - Buku Lopatulika12 Pakuti Iye wofuna chamwazi awakumbukira; saiwala kulira kwa ozunzika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Pakuti Iye wofuna chamwazi awakumbukira; saiwala kulira kwa ozunzika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Paja Iye amachitira chifundo anthu ozunzika, salephera kumva kulira kwao ndipo amalanga anthu oŵazunzawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pakuti Iye amene amabwezera chilango akupha anzawo wakumbukira; Iye salekerera kulira kwa ozunzika. Onani mutuwo |