Masalimo 9:11 - Buku Lopatulika11 Imbirani zoyamika Yehova, wokhala ku Ziyoni; lalikirani mwa anthu ntchito zake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Imbirani zoyamika Yehova, wokhala ku Ziyoni; lalikirani mwa anthu ntchito zake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Imbani nyimbo zotamanda Chauta amene amakhala ku Ziyoni. Lalikani za ntchito zake kwa anthu a mitundu yonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Imbani nyimbo zamatamando kwa Yehova, ali pa mpando waufumu mu Ziyoni; lengezani pakati pa mitundu ya anthu zimene wachita. Onani mutuwo |