Koma iwo adzabweranso kuno mbadwo wachinai: pakuti mphulupulu za Aamori sizinakwaniridwe.
Eksodo 13:4 - Buku Lopatulika Mutuluka lero lino mwezi wa Abibu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mutuluka lero lino mwezi wa Abibu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mukuchoka ku Ejipito pa tsiku lalero, mwezi uno wa Abibu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pa tsiku la lero mwezi uno wa Abibu, mukutuluka mʼdziko la Igupto. |
Koma iwo adzabweranso kuno mbadwo wachinai: pakuti mphulupulu za Aamori sizinakwaniridwe.
Uzisunga chikondwerero cha Mkate wopanda chotupitsa; masiku asanu ndi awiri uzidya mkate wopanda chotupitsa, monga ndinakuuza, nyengo yoikika, mwezi wa Abibu, pakuti m'menemo unatuluka mu Ejipito; koma asaoneke munthu pamaso panga opanda kanthu;
Uzisunga chikondwerero cha Mkate wopanda chotupitsa. Uzidya mkate wopanda chotupitsa masiku asanu ndi awiri, monga ndakuuza pa nthawi yonenedwa, m'mwezi wa Abibu; pakuti mwezi wa Abibu unatuluka mu Ejipito.
Ndipo ndinakhazikitsanso nao chipangano changa, kuwapatsa dziko la Kanani, dziko la maulendo ao, anali alendo m'mwemo.