Eksodo 12:2 - Buku Lopatulika2 Mwezi uno uzikhala kwa inu woyamba wa miyezi; muziuyesa mwezi woyamba wa chaka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Mwezi uno uzikhala kwa inu woyamba wa miyezi; muziuyesa mwezi woyamba wa chaka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 “Mwezi uno udzakhala mwezi wanu woyambira chaka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Mwezi uno uzikhala mwezi wanu woyamba wa chaka. Onani mutuwo |