Eksodo 13:4 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Pa tsiku la lero mwezi uno wa Abibu, mukutuluka mʼdziko la Igupto. Onani mutuwoBuku Lopatulika4 Mutuluka lero lino mwezi wa Abibu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Mutuluka lero lino mwezi wa Abibu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mukuchoka ku Ejipito pa tsiku lalero, mwezi uno wa Abibu. Onani mutuwo |
“Muzichita Chikondwerero cha Buledi wopanda Yisiti. Kwa masiku asanu ndi awiri muzidya buledi wopanda yisiti monga ndinakulamulirani. Muzichita zimenezi mwezi wa Abibu pa nthawi yomwe ndayika, pakuti mʼmwezi umenewu munatuluka mʼdziko la Igupto. “Pasapezeke munthu wobwera pamaso panga wopanda kanthu mʼmanja.