Chikakomera mfumu, atuluke mau achifumu pakamwa pake, nalembedwe m'malamulo a Apersiya ndi Amediya, angasinthike, kuti Vasiti asalowenso pamaso pa mfumu Ahasuwero; ndi mfumu aninkhe chifumu chake kwa mnzake womposa iye.
Danieli 6:9 - Buku Lopatulika Momwemo mfumu Dariusi anatsimikiza cholembedwa ndi choletsacho. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Momwemo mfumu Dariusi anatsimikiza cholembedwa ndi choletsacho. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Choncho mfumu Dariyo anasindikizapo dzina lake pa lamuloli. |
Chikakomera mfumu, atuluke mau achifumu pakamwa pake, nalembedwe m'malamulo a Apersiya ndi Amediya, angasinthike, kuti Vasiti asalowenso pamaso pa mfumu Ahasuwero; ndi mfumu aninkhe chifumu chake kwa mnzake womposa iye.
Siyani munthu, amene mpweya wake uli m'mphuno mwake; chifukwa m'mene awerengedwamo ndi muti?