Danieli 6:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Choncho mfumu Dariyo anasindikizapo dzina lake pa lamuloli. Onani mutuwoBuku Lopatulika9 Momwemo mfumu Dariusi anatsimikiza cholembedwa ndi choletsacho. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Momwemo mfumu Dariusi anatsimikiza cholembedwa ndi choletsacho. Onani mutuwo |