Yohane 7:53 - Buku Lopatulika Ndipo anamuka munthu yense kunyumba yake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anamuka munthu yense kunyumba yake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamenepo anthu onse adabwerera kwao.] Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kenaka onse anachoka, napita kwawo. |
Indedi, kuzaza kwake kwa munthu kudzakulemekezani; chotsalira cha kuzazaku mudzachiletsa.
Olimba mtima chifunkhidwa chuma chao, agona tulo tao; amuna onse amphamvu asowa manja ao.
Anayankha nati kwa iye, Kodi iwenso uli wotuluka mu Galileya? Santhula, nuone kuti mu Galileya sanauke mneneri.