Masalimo 76:5 - Buku Lopatulika5 Olimba mtima chifunkhidwa chuma chao, agona tulo tao; amuna onse amphamvu asowa manja ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Olimba mtima chifunkhidwa chuma chao, agona tulo tao; amuna onse amphamvu asowa manja ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Mudalanda zofunkha za anthu olimba mtima, mudaŵagonetsa tulo tofa nato, ankhondo onse sankatha kuchita kanthu ndi manja ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Anthu owuma mtima amagona atalandidwa chuma, Iwowo amagona tulo tawo totsiriza; palibe mmodzi wamphamvu amene angatukule manja ake. Onani mutuwo |