Masalimo 76:4 - Buku Lopatulika4 Inu ndinu wakuunikira, ndi womveka wakuposa mapiri muli achifwamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Inu ndinu wakuunikira, ndi womveka wakuposa mapiri muli achifwamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Inu Mulungu, mukuwonetsa ulemerero ndi mphamvu kupambana mapiri a zofunkha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Wolemekezeka ndinu, wamphamvu kuposa mapiri amene ali ndi nyama zambiri. Onani mutuwo |