Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 76:3 - Buku Lopatulika

3 Pomwepo anathyola mivi ya pauta; chikopa, ndi lupanga, ndi nkhondo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Pomwepo anathyola mivi ya pauta; chikopa, ndi lupanga, ndi nkhondo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Kumeneko adathyola mivi youluzika, zishango, malupanga ndi zida zonse zankhondo za adani ake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Kumeneko Iye anathyola mivi yowuluka, zishango ndi malupanga, zida zankhondo. Sela

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 76:3
9 Mawu Ofanana  

Ndipo Melkizedeki mfumu ya ku Salemu, anatuluka nao mkate ndi vinyo: iye ndiye wansembe wa Mulungu Wamkulukulu.


Ndipo pofika Yehosafati ndi anthu ake kutenga zofunkha zao, anapezako chuma chambiri, ndi mitembo yambiri ndi zipangizo zofunika, nadzifunkhira, osakhoza kuzisenza zonse; nalimkutenga zofunkhazo masiku atatu, popeza zinachuluka.


Ndipo Yehova anatuma wamthenga amene anaononga ngwazi zamphamvu zonse, ndi atsogoleri, ndi akazembe, kuchigono cha mfumu ya Asiriya. Nabwerera iye ndi nkhope yamanyazi kudziko lake. Ndipo atalowa m'nyumba ya mulungu wake, iwo otuluka m'matumbo mwake anamupha ndi lupanga pomwepo.


Aletsa nkhondo ku malekezero a dziko lapansi; athyola uta, nadula nthungo; atentha magaleta ndi moto.


Pakuti Iye wofuna chamwazi awakumbukira; saiwala kulira kwa ozunzika.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa