Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 76:2 - Buku Lopatulika

2 Msasa wake unali mu Salemu, ndipo pokhala Iye mu Ziyoni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Msasa wake unali m'Salemu, ndipo pokhala Iye m'Ziyoni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Hema lake adalimanga ku Yerusalemu. Malo ake okhalamo ali kumeneko ku Ziyoni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Tenti yake ili mu Salemu, malo ake okhalamo mu Ziyoni.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 76:2
9 Mawu Ofanana  

Ndipo Melkizedeki mfumu ya ku Salemu, anatuluka nao mkate ndi vinyo: iye ndiye wansembe wa Mulungu Wamkulukulu.


Koma ndinasankha Yerusalemu, kuti dzina langa likhale komweko; ndinasankhanso Davide akhale mfumu ya anthu anga Israele.


Chifukwa kuti pa tsiku la tsoka Iye adzandibisa mumsasa mwake, adzandibisa mkati mwa chihema chake; pathanthwe adzandikweza.


Phiri la Ziyoni, chikhalidwe chake nchokoma kumbali zake za kumpoto, ndilo chimwemwe cha dziko lonse lapansi, mzinda wa mfumu yaikulu.


Imbirani zoyamika Yehova, wokhala ku Ziyoni; lalikirani mwa anthu ntchito zake.


Tafuula, takuwa iwe, wokhala mu Ziyoni, chifukwa Woyera wa Israele wa m'kati mwako ali wamkulu.


Wachotsa mwamphamvu dindiro lake ngati la m'munda; waononga mosonkhanira mwake; Yehova waiwalitsa anthu msonkhano ndi Sabata mu Ziyoni; wanyoza mfumu ndi wansembe mokwiya mwaukali.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa