Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 76:1 - Buku Lopatulika

1 Mulungu adziwika mwa Yuda, dzina lake limveka mwa Israele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Mulungu adziwika mwa Yuda, dzina lake limveka mwa Israele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Mulungu ndi wodziŵika m'dziko la Yuda, dzina lake ndi lolemekezeka mu Israele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Mulungu amadziwika mu Yuda; dzina lake ndi lotchuka mu Israeli.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 76:1
18 Mawu Ofanana  

Pakufuula ine mundiyankhe, Mulungu wa chilungamo changa; pondichepera mwandikulitsira malo. Ndichitireni chifundo, imvani pemphero langa.


Mulungu wa milungu, Yehova, wanena, aitana dziko lapansi kuyambira kutuluka kwa dzuwa kufikira kulowa kwake.


Ndipulumutseni, Mulungu, mwa dzina lanu, ndipo mundiweruze ndi mphamvu yanu.


Imvani mfuu wanga, Mulungu; mverani pemphero langa.


Atichitire chifundo Mulungu, ndi kutidalitsa, atiwalitsire nkhope yake;


Chifukwa chake ndilamulira kuti anthu ali onse, mtundu uliwonse, ndi a manenedwe ali onse, akunenera molakwira Mulungu wa Sadrake, Mesaki, ndi Abedenego, adzadulidwa nthulinthuli, ndi nyumba zao zidzasanduka dzala; popeza palibe mulungu wina akhoza kulanditsa motero.


Pakuti popita, ndi kuona zinthu zimene muzipembedza, ndipezanso guwa la nsembe lolembedwa potere, KWA MULUNGU WOSADZIWIKA. Chimene muchipembedza osachidziwa, chimenecho ndichilalikira kwa inu.


Koma ngati iwe unenedwa Myuda, nukhazikika palamulo, nudzitamandira pa Mulungu,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa