Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 75:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo ndidzatseteka nyanga zonse za oipa; koma nyanga za wolungama zidzakwezeka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo ndidzatseteka nyanga zonse za oipa; koma nyanga za wolungama zidzakwezeka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Iye adzaphwanya mphamvu za anthu onse oipa, koma adzaonjezera mphamvu za anthu okhulupirira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Ndidzadula nyanga za onse oyipa koma nyanga za olungama zidzakwezedwa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 75:10
8 Mawu Ofanana  

Mamawa onse ndidzadula oipa onse a m'dziko; kuduliratu onse akuchita zopanda pake kumzinda wa Yehova.


Ndipo anakweza nyanga ya anthu ake, chilemekezo cha okondedwa ake onse; ndiwo ana a Israele, anthu a pafupi pa Iye. Aleluya.


Popeza Inu ndinu ulemerero wa mphamvu yao; ndipo potivomereza Inu nyanga yathu idzakwezeka.


Koma munakweza nyanga yanga ngati ya njati; anandidzoza mafuta atsopano.


Nyanga ya Mowabu yaduka, ndipo wathyoka mkono wake, ati Yehova.


Ndipo Iye anatikwezera ife nyanga ya chipulumutso, mwa fuko la Davide mwana wake.


Ndipo Hana anapemphera, nati, Mtima wanga umyuka mokondwera kwa Yehova, nyanga yanga yakwezeka mwa Yehova; pakamwa panga pakula kwa adani anga; popeza ndikondwera m'chipulumutso chanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa