Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 21:6 - Buku Lopatulika

6 ndi kulawirana; ndipo tinalowa m'ngalawa, koma iwo anabwera kwao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 ndi kulawirana; ndipo tinalowa m'ngalawa, koma iwo anabwera kwao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Ndipo titatsazikana, ife tidakaloŵa m'chombo, iwowo nkumabwerera kwao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Titatsanzikana, tinalowa mʼsitima ija, iwowo anabwerera ku nyumba zawo.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 21:6
6 Mawu Ofanana  

Ndipo iye ananyamuka, nadza kwa atate wake. Koma pakudza iye kutali atate wake anamuona, nagwidwa chifundo, nathamanga, namkupatira pakhosi pake, nampsompsonetsa.


Anadza kwa zake za Iye yekha, ndipo ake a mwini yekha sanamlandire Iye.


Onani ikudza nthawi, ndipo yafika, imene mudzabalalitsidwa, yense ku zake za yekha, ndipo mudzandisiya Ine pa ndekha. Ndipo sindikhala pa ndekha, chifukwa Atate ali pamodzi ndi Ine,


Pamene ananena kwa wophunzirayo, Taona, amai wako. Ndipo kuyambira ora lomweli wophunzirayo ananka naye kwao.


Ndipo anamuka munthu yense kunyumba yake.


ndinalibe mpumulo mu mzimu wanga, posapeza ine Tito mbale wanga; koma polawirana nao ndinanka ku Masedoniya.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa