Numeri 2:7 - Buku Lopatulika Ndi fuko la Zebuloni: kalonga wa ana a Zebuloni ndiye Eliyabu mwana wa Heloni. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi fuko la Zebuloni: kalonga wa ana a Zebuloni ndiye Eliyabu mwana wa Heloni. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono pabwere fuko la Zebuloni, limene mtsogoleri wake ndi Eliyabu mwana wa Heloni, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Lotsatira lidzakhala fuko la Zebuloni. Mtsogoleri wa gulu la Zebuloni ndi Eliabu mwana wa Heloni. |
Ndipo khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zinai kudza mazana anai.
Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zisanu ndi ziwiri kudza mazana anai.
ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Eliyabu mwana wa Heloni.