Numeri 7:24 - Buku Lopatulika24 Tsiku lachitatu kalonga wa ana a Zebuloni, ndiye Eliyabu mwana wa Heloni: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Tsiku lachitatu kalonga wa ana a Zebuloni, ndiye Eliyabu mwana wa Heloni: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Tsiku lachitatu linali la Eliyabu mwana wa Heloni mtsogoleri wa Azebuloni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Pa tsiku lachitatu, Eliabu mwana wa Heloni, mtsogoleri wa Azebuloni, anabweretsa chopereka chake. Onani mutuwo |