Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 2:7 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Lotsatira lidzakhala fuko la Zebuloni. Mtsogoleri wa gulu la Zebuloni ndi Eliabu mwana wa Heloni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

7 Ndi fuko la Zebuloni: kalonga wa ana a Zebuloni ndiye Eliyabu mwana wa Heloni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndi fuko la Zebuloni: kalonga wa ana a Zebuloni ndiye Eliyabu mwana wa Heloni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Tsono pabwere fuko la Zebuloni, limene mtsogoleri wake ndi Eliyabu mwana wa Heloni,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 2:7
7 Mawu Ofanana  

Eliabu mwana wa Heloni, kuchokera ku fuko la Zebuloni,


Eliabu mwana wa Heloni ndiye anali mtsogoleri wa fuko la Zebuloni.


Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 54,400.


Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 57,400.


Pa tsiku lachitatu, Eliabu mwana wa Heloni, mtsogoleri wa Azebuloni, anabweretsa chopereka chake.


ndi ngʼombe ziwiri, nkhosa zazimuna zisanu, mbuzi zazimuna zisanu ndi ana ankhosa aamuna asanu a chaka chimodzi, nsembe yachiyanjano. Ichi chinali chopereka cha Eliabu mwana wa Heloni.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa