Numeri 2:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zinai kudza mazana anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zinai kudza mazana anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 ndipo ankhondo ake ngokwanira 54,400. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 54,400. Onani mutuwo |