Numeri 2:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo iwo akumanga mahema ao poyandikizana naye ndiwo a fuko la Isakara; ndipo kalonga wa ana a Isakara ndiye Netanele mwana wa Zuwara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo iwo akumanga mahema ao poyandikizana naye ndiwo a fuko la Isakara; ndipo kalonga wa ana a Isakara ndiye Netanele mwana wa Zuwara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Amene amange pafupi ndi fuko lake akhale a fuko la Isakara. Mtsogoleri wa fuko la Isakaralo ndi Netanele mwana wa Zuwara, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Fuko la Isakara lidzamanga pafupi ndi Yuda. Mtsogoleri wa gulu la Isakara ndi Netanieli mwana wa Zuwara. Onani mutuwo |