Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 10:16 - Buku Lopatulika

16 Ndi gulu la fuko la ana a Zebuloni panali Eliyabu mwana wa Heloni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Ndi gulu la fuko la ana a Zebuloni panali Eliyabu mwana wa Heloni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Mtsogoleri wa gulu la fuko la Zebuloni anali Eliyabu mwana wa Heloni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Eliabu mwana wa Heloni ndiye anali mtsogoleri wa fuko la Zebuloni.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 10:16
4 Mawu Ofanana  

Wa Zebuloni, Eliyabu mwana wa Heloni.


Ndi pa gulu la fuko la ana a Isakara panali Netanele mwana wa Zuwara.


Ndipo anagwetsa chihema; ndi ana a Geresoni, ndi ana a Merari, akunyamula chihema, anamuka nacho.


Tsiku lachitatu kalonga wa ana a Zebuloni, ndiye Eliyabu mwana wa Heloni:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa