Numeri 10:15 - Buku Lopatulika15 Ndi pa gulu la fuko la ana a Isakara panali Netanele mwana wa Zuwara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndi pa gulu la fuko la ana a Isakara panali Netanele mwana wa Zuwara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Mtsogoleri wa gulu la fuko la Isakara anali Netanele mwana wa Zuwara. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Mtsogoleri wa gulu la fuko la Isakara anali Netanieli mwana wa Zuwara, Onani mutuwo |